Wa misala anaona nkhondo: Oyimba Che Wikise amene amadziwika kwambiri ndi nyimbo zowoneka ngati zoduka mutu koma za uthenga wa mphamvu, walangiza abambo onse a mvula za kale omwe samaugwira mtima akawona dilesi la ma buthu obadwa zaka za m’ma 2000 mpaka alowemo, kuti asamale apwetekedwa komaso ayalutsidwa. Loweluka pa 3 February, 2024, Wikise yemwe […]
The post Ana a m’ma 2000 akupwetekani – Wikise walangiza zimdya makanda appeared first on Malawi 24.