Oba ndalama za boma adwala nthenda zikuluzikulu – watero mneneri Mbewe

…wati boma la Tonse lidzipita, ndi la bodza Mtsogoleri wa gulu la Freedom of Worship and Economic Liberation (FOWEL) mneneri David Mbewe walavula zakukhosi powauza atsogoleri a mgwirizano wa Tonse kuti ndalama za boma zomwe akuba adwala nazo nthenda zikuluzikulu, ndipo wati azilavula popita zipatala zakunja. Mneneri Mbewe amayankhula izi Loweruka usiku pamene mpingo wawo […]

The post Oba ndalama za boma adwala nthenda zikuluzikulu – watero mneneri Mbewe appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください