Zitsulo kunolana: Bushiri athandiza mneneri Habakkuk kupeza  K1 miliyoni 

Khama lipindura: Mneneri Habakkuk yemwe, pafupipafupi, wakhala akupempha Shepherd Bushiri kuti amuthandize ndi K1 miliyoni yokha, waona ngati kutulo pomwe wapatsidwa K6 miliyoni ndi mneneri nzakeyu. Habakkuk yemwe dzina lake lenileni ndi Stanford Sinyangwe, sadzayiwala tsiku La mulungu pa 5 May, 2024  kamba koti mneneri Bushiri anamuchitira chinthu chomwe wakhala akumupempha.  Patsikuli, Bushiri  amachititsa mapemphero […]

The post Zitsulo kunolana: Bushiri athandiza mneneri Habakkuk kupeza  K1 miliyoni  appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください