Zipatala zinayi zomwe zikumangidwa ku Neno zichepetsa mavuto a zaumoyo

Boma mothandizidwa ndi Bungwe la Global Fund likumanga zipatala zinayi Zing’ono zing’ono Boma la Neno. Zipatalazi zikumangidwa kumadera ovuta kufikirako omwe alikutali kwambiri ndi zipatala za Boma. Zipatala zomwe zikumangidwazi ndi Gonthi, Godeni, Feremu ndi kambale ndipo zikumangidwa ndi ndalama zosachepera 1 billion Malawi kwacha. Polakhula ndi Malawi24, Mayi m’modzi ochokera m’mudzi mwa Felemu, Afinesi […]

The post Zipatala zinayi zomwe zikumangidwa ku Neno zichepetsa mavuto a zaumoyo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください