Pamene masiku akuthera kuchitseko kuti dziko lino lizachititse chisankho china mu 2025, Ras David Chikomeni Chirwa walengeza kuti adzapikisana nawo pomwe mtsogoleri wakale a Peter Mutharika ati anthu ambiri akuwapempha kuti adzaimeso. Nkhaniyi yayamba ndi a Mutharika omwe la mulungu pa 10 July anauza wailesi ya Voice of America kuti a Malawi ambiri kuphatikizapo atsogoleri […]
The post Zilikoliko 2025: Mutharika, Chikomeni awonetsa chidwi chodzaimanso appeared first on Malawi 24.