Zigoli 7 za Moyale Barracks zatutumutsa anthu, Blue Eagles yakamang’ala

Timu ya Moyale Barracks yomwe imafunika kugoletsa zigoli zisanu ndi ziwiri (7) kuti isawonetsedwe nsana wa njira muligi yaikulu ya TNM, yadabwitsa anthu pomwe inakwanitsa kuchinya zigoli zonsezi pomwe imasewera ndi timu ya Red Lions ndipo timu ya Blue Eagles ikuganiza kuti panayenda chinyengo ndipo yakasuma. Kunali mpira wa magazi la Mulungu lapitali pomwe ma […]

The post Zigoli 7 za Moyale Barracks zatutumutsa anthu, Blue Eagles yakamang’ala appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください