Zidzukulu zanjatwa popha gogo wawo pa nkhani za ufiti

Zaka zapitazo Gogo Elisa Supuni ya zaka 73 m’boma la Mulanje inabala ana, ndipo ana awowo anabalaso ana, koma mphuno salota gogowa sanadziwe kuti adzaphedwa ngati njoka ndi zidzukulu zawozi powaganizira kuti gogowa anapha m’matsenga chidzukulu chawo china. Tikukukamba pano zidzukulu zitatu zili m’manja mwa apolisi. Watsimikiza za kumangidwa kwa zidzukuluzi ndi ofalitsa nkhani pa […]

The post Zidzukulu zanjatwa popha gogo wawo pa nkhani za ufiti appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください