Zibwana zofinyana pakhosi: nthabwala za Ichocho zikhumudwitsa a Malawi

…apolisi awayendere — katswiri wa chitetezo Ena akukanika kuyankhula momasuka chifukwa akuopa kukupidwa makofi. Ena ndiye angomasula. Koma a Malawi ochuluka aoneka odabwa ndi vidiyo imene watulutsa phona wa mu mzinda wa Blantyre, Ichocho, yolengeza kuti wayamba kufwamba anthu. Malinga ndi kanema amene anthu akugawana, Ichocho ndi gulu lake la ziphona akhala ngati zigawenga za […]

The post Zibwana zofinyana pakhosi: nthabwala za Ichocho zikhumudwitsa a Malawi appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください