Eeyo! Tiyeni! Tiyeni! Tiyeni: ngakhale kuti “K100 miliyoni sindalama”, koma Dorothy Shonga akuyenera kuchengetera bwenzi lake Zeze Kingston ngati dzira kamba koti Jetu waopseza kutsomphora chikhwayacho. Ndi mkazi uti samafuna mamuna otulutsa K500, 000 yandiwo pa sabata? Gogo Jetu abwera ndi mkokomo komaso moto omwe ukulilima kowopsa ndipo ngakhale kampani yozimitsa motoyo ikupeleweledwa nthanana kuti […]
The post “Zeze ndili naye pulani” – Jetu achenjeza Cash Madam appeared first on Malawi 24.