Potsatira kugwa mphamvu kwa ndalama ya Kwacha, bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA), lakweza mitengo ya magetsi ndi mafuta a galimoto ndi pafupipafupi 45 Kwacha pa 100 Kwacha iliyonse ndipo izi zikuchitika pomwe mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ali kunja. Malingana ndi kalata yomwe bungwe la MERA yatulutsa usiku wa lachinayi, kukwera […]
The post Zayambika: Mafuta a galimoto, magetsi akwezedwa mtengo appeared first on Malawi 24.