Zayambika ku manoma: alepherana ndi Tigers

Mwayidziwa bwino nyimbo ya mwana ndi mwana imene amakonda kuimba ma Palestina? Kukhala ngati mwana wake amanena achabale awo a Mighty Mukuru Wanderers kapena kuti Manoma. Zawaonekera lero atalepherana ndi timu ya Mighty Tigers. Atayamba bwino ligi popambana masewero awo atatu kuti akhale pamwamba kwa sabata zitatu, nyerere lero zakumbutsidwa kuti ligi si zibwana. Pa […]

The post Zayambika ku manoma: alepherana ndi Tigers appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください