Zandikwana! Enock Chihana akuti amanga yekha chiliza cha abambo ake: Boma latinamiza mokwanira

Mtsogoleri wa Aford a Enock Chihana ati pa 6 April chaka chino akhala akukhazikitsq ntchito yomanga chiliza cha malemu Chakufwa Chihana omwe anali bambo ake. Iwo ati akulu akulu ena aku mabungwe monga a United Nations komanso mtsogoleri wakale wa dziko lino Dr Bakili Muluzi awalonjeza kuti akayamba ntchito yomanga chilizachi adzawathandiza. Iwo alankhula izi […]

The post Zandikwana! Enock Chihana akuti amanga yekha chiliza cha abambo ake: Boma latinamiza mokwanira appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください