Zachitika: Paul Banda walandira K14.5m yomwe a Malawi asonkha kuti ithandize malipiro akuchipatala

Oyibma Paul Banda lero walandira ndalama zokwana K14.5 miliyoni zomwe a Malawi, motsogozedwa ndi Onjezani Kenani, asonkha kuti zimuthandize kulandira chithandizo kuchipatala. Katswiri oyimbayu akudwala matenda a ipso ndipo wapatsidwa ndalama zi ku nyumba kwake kwa Chatha ku Chileka mu mzinda wa Blantyre.Mukuyankhula kwawo akuti kuthokoza kwake kukuwavuta chifukwa samayembekezera zoterezi. “Zikanakhala a Malawi timathandizana […]

The post Zachitika: Paul Banda walandira K14.5m yomwe a Malawi asonkha kuti ithandize malipiro akuchipatala appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください