Zachitika! A polisi ndi akhonsolo ya Lilongwe agumula masitolo omangidwa mmanda ku Area 25

Ku m’banda kucha lero loweluka achitetezo komanso akhonsolo ya mzinda  wa Lilongwe, agumula komanso kufwafwaniza masitolo omwe anthu adamanga m’manda ku Nsungwi ku Area 25. Malingana ndi anthu omwe anaona izi zikuchitika, ati achitetezowa anafika chama 1 koloko m’banda kucha, ndipo anatseka nseu wa Nsungwi kuyamba kugwira ntchito yawo. Ena mwa omwe tayankhulana nawo pamalowa […]

The post Zachitika! A polisi ndi akhonsolo ya Lilongwe agumula masitolo omangidwa mmanda ku Area 25 appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください