Za nkhumba ija zatha bwino, timathandiza zonse – atelo apolisi

Pomwe anthu ena amadzudzula mkulu wa ku Mulanje yemwe anatengera ku polisi nkhumba yake yomwe imakanika kufa, apolisi ati panalibe vuto kutelo ndipo alimbikitsa anthu kuti adzipita ndi nkhani zawo za mtundu uli onse adzathandizidwa bwino. Lamulungu lapitali pa 14 January, 2024, anthu ochuluka anakhamukira pa polisi ya Mulanje kukaona nkhumba yomwe imakanika kufa pomwe […]

The post Za nkhumba ija zatha bwino, timathandiza zonse – atelo apolisi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください