Odya naye mbale imodzi ndiye okupelekayo; ndipo monga m’mene Yudasi anapelekera Yesu kuti aphedwe, mchimwene wa malemu Agnes Katengeza wavomera kuti anatenga gawo lalikulu pa imfa ya m’bale wakeyo yemwe amakhala naye nyumba imodzi. Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu atsimikiza zakumangidwa kwa Amos Katengeza wa zaka 27, yemwe akuti ndi mchimwene wa […]
The post Yudasi! Mchimwene wavomera kuti anatenga gawo pa imfa ya Agnes Katengeza appeared first on Malawi 24.