Yawalakwira Cash Madam… a bwalo ati ali ndi mulandu

Pamene dziko linatangwa ndi kumangidwa kwa Mayi Chizuma, bwalo ku Lilongwe linatangwa ndi kuzenga milandu Mayi Dorothy Shonga komanso mkulu wakale wa MERA, a Collins Magalasi. Ndipo agwa nayo kale round yoyamba. Oweluza milandu a Patrick Chirwa apeza kuti a Shonga ndi a Magalasi, kudza anthu ena awiri, ali ndi milandu yoti ayankhe yokhudzana ndi […]

The post Yawalakwira Cash Madam… a bwalo ati ali ndi mulandu appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください