Yapamphanthidwa ngati wakuba foni

Kunali mkoke mkoke lero mu Tnm Super League pamene anyamata amakudzulana nthenga, kugwalulana zibwano, kuchotsana chimbenene. Uyu ndi tsatanetsane wamomwe lero masewero athera. Mighty Wanderers yalepherana ndi timu ya Bangwe All Stars, ndipo masewero athera 0 kwa 0. Asilikali a Kamuzu Barracks akuntha ndikufinya kholingo anyamata a Civo Service United ndi Zigoli ziwiri kwa chimodzi. […]

The post Yapamphanthidwa ngati wakuba foni appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください