Yambani kulongedza ife tidzakonze zinthu, Kabambe wauza a Chakwera

M’modzi wa anthu omwe akufuna utsogoleri ku chipani cha DPP a Dalitso Kabambe awuza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti ayambe kulongedza popeza kuthekera kokonza zinthu alibe. Malingana ndi a Kabambe omwe anakhalapo mkulu wa bank yaikilu ya Reserve, iwo ali okonzeka kuzakonza zinthu m’dziko muno. Mukulemba kwawo pa tsamba la mchezo m’mawa […]

The post Yambani kulongedza ife tidzakonze zinthu, Kabambe wauza a Chakwera appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください