Kampani yogulitsa malo ya Eagles Real Estate Consultants yapeleka plot kwa oyimba Jetu yemwe dzina lake lenileni ndi Christina Kholiyo pomulimbikitsa pa ntchito yake yoyimba komanso kusangalatsa anthu. Mkulu owona za malonda ku kampaniyi a Roshan Thole wati plot-yi yomwe ili ku Lilongwe ku Airwing ndi ya ndalama zosachepra K6 Million Kwacha ndipo iyi ndi […]
The post Woyimba wazaka 74, Jetu, alandira plot kuchokera ku Eagles Real Estate Consultants appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.