Woyimba wodziwika bwino Maskal, yemwe akukhala m’dziko la United States of America wafika m’dziko muno kudzera ku bwalo la ndege la Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe. Maskal, yemwe amadziwika ndi nyimbo zake monga ‘Udalire’, akuyembekezeka kukhala nawo pa phwando la maimbidwe ku Illusionz mu mzinda wa Lilongwe Loweruka. Phwando la maimbidweli likusangalalira Nde’feyo Entertainment yomwe […]
The post Woyimba Maskal wafika mudziko muno Kuchoka USA kuzayimba ku Chiphwando ku Illusionz loweluka appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.