Ndaine Game wa zaka 42, yemwe anali mu chaka chachiwiri ku sukulu ya anamwino ya Malamulo, wadzimangilira lachisanu masana. Apolisi m’boma la Thyolo atsimikiza za imfa ya a Game omwe amaphnzira za mankhwala ku Malamulo. Mkulu wa apolisi, a Francis Chisoti, wati Game wasiya kalata yofotokoza za kudziphaku. Malingana ndi a Chisoti, Game yemwe ankachokera […]
The post Wophunzira ku sukulu ya anamwino wadzipha appeared first on Malawi 24.