Pamene luso lojambula limayang’anilidwa pansi ndi anthu ambiri, nzika ya ku Malawi mu dziko la Zambia, Wonder Kumbikano yaponyera kwakuya luso lake lojambula kugwiritsa ntchito pensulo. Nyamatayi yemwe zaka zake zakubadwa ndi makumi atatu ndi ziwiri wayipatsa moto pakuti akuphunzira kugwiritsa ntchito zipangizo zojambulira za makono monga blending stump, chacoal pencil, tombo mono zero eraser […]
The post Wonder kumbikano akukuza luso lojambula ku Zambia appeared first on Malawi 24.