Wode Maya wavula chinyawu; watulutsa kanema ali ku ndagala

Pomwe anthu omwe sizikuwakhudza amaletsedwa kupita ku malo alionse opangira chinamwali cha a yao, ndagala, anthu adzidzimuka kuti mlendo Wode Maya wa ku Ghana anakalowako mpaka kujambula kanema yomwe watulutsa pano. Mlendo odza nkalumo kakuthwayu yemwe dzina lake lenileni ndi Berthold Winkler, posachedwapa anali m’dziko muno paulendo wake odzasilira zachilengedwe zomwe dziko lino linadalitsika nazo, […]

The post Wode Maya wavula chinyawu; watulutsa kanema ali ku ndagala appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください