Mtsogoleri wa chipani cha DPP, a Peter Mutharika amene owakonda amangoti APM, akuyembekezereka kugwedeza mzinda wa Blantyre mawa lino pa 12 May. A Mutharika amene akhala nthawi osachititsa msonkhano wandale alengeza kuti akhala pa Njamba Freedom Park. Malinga ndi tsamba lawo la Facebook, iwo ati akubwera pa Njamba kuti afotokozere a Malawi mfundo zawo za […]
The post Wayamba kampeni Mutharika, ali pa Njamba mawa lino appeared first on Malawi 24.