Uja anati menya galu kuti udziwe mbuye wake n’kutheka adalinga izi. Patangotha maola ochepa boma litatafulira boma la Amereka kamba koletsa anthu ena kupita ku dzikolo kamba ka katangale, naye tate wawo Chakwera wayankhulapo. Iye wati boma la Amereka lilekeletu zoletsa a Malawi oganiziridwa katangale kupita mu dzikolo. Polankhula mu mzinda wa Lilongwe, a Chakwera […]
The post Watulukira mbuyake wa galu: Chakwera wati Amereka ilekeretu zoletsa a Malawi kupita ku dzikolo appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 