Mzika ya dziko lino a Eddie Gaddafi General Longwe omwe amakhala mdziko la Asia ati alindichidwi chopikisana nawo pazisankho za mtsogoleri wadziko lino zomwe zikuyembekezeka kuchitika chaka chamawa ngati oyima pawokha. Agadafi auza Nyasatimes kuti iwo ndiwokonzeka kuombola amalawi omwe pakadali pano akukumana ndimavuto osiyanasiyana mu ulamuliro wa presidenti Dr. Lazarus Chakwera. Iwo ati ali […]
The post Watulukira Gaddafi General Longwe! Akuti muvoteleni kuti a Malawi mulawe kusintha appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.