Inu amene mukumapeza mwayi otsukuluza mkamwa pa nkhani zokhudza mtsogoleri wa dziko lino a Chakwera yambani kuyenda mosamala. Ayamba kunjata anthu kunja kuno ati chifukwa chonyoza a Chakwera. A Sainani Nkhoma a ku Dowa akuyembekezeka kumva chigamulo chawo sabata la mawa pamene a bwalo apeza kuti mkuluyu anatsukuluza mkamwa pothilira ndemanga pa nkhani yokhudza a […]
The post Watsekeledwa wina chifukwa chonyoza Chakwera pa WhatsApp appeared first on Malawi 24.