Zitangodziwika kuti Fleetwood Haiya ndi amene wapambana chisankho cha mtsogoleri wa bungwe la FAM, kunatekeseka ku Ntaja m’boma la Machinga anthu anakhamukira ku nyumba ya mwana wawoyu kukavina kamba kowachotsa manyazi. Lero loweruka a Haiya apambana chisankho chomwe chimachitika ku bungwe loyendetsa mpira wa miyendo la Football Association of Malawi ndipo iwowa agonjetsa a Walter […]
The post “Watichotsa manyazi” – khamu lakavina ku nyumba kwa Haiya appeared first on Malawi 24.