A Maxwell James a zaka 23 zakubadwa akusungidwa mchitokosi cha apolisi ku Phalombe kamba kopezeka ndi ndalama zachinyengo zokwana K240,000. Nkhani yonse ikuti pa 9 December a James adapita ku msika wawukulu wa Mulomba komwe iwo ankafuna kuyika ndalamazo mu lamya kudzera kwa ejenti wa Mpamba komanso Aitel Money. Ejent atayika ndalama zokwana K155,000 mu […]
The post Wathilidwa unyolo kamba kopezeka ndi ma K5,000 okwana K240,000 achinyengo appeared first on Malawi 24.