Ngati wina kundendeko amakonzekera kuti tsiku lina adzakhala mesho wa a Saulos Chilima asiyiletu. Milandu yawo yonse ija a boma aithetsa. Tsopano ndi mfulu. Bwalo la milandu lero pa 6 May lavomereza pempho lochoka kwa mkulu oyimba milandu oti milandu ya katangale yokhudza wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino ithe. Izi zili mu chikalata chimene […]
The post Watha basi! Boma la Chakwera lathetsa mlandu wa Chilima appeared first on Malawi 24.