Wapulumuka pamene khoti lati msungwana amati anagona nayeyo simwana

Njonda ina yazaka 30 zakubadwa, yapulumukira mkamwa mwa njovu pamene bwalo lamilandu ku Kasungu lamupeza osalakwa pa mlandu omwe amamuzenga ogonana ndi mtsikana yemwe amati ndi wa zaka 16. Mkuluyu yemwe dzina lake ndi Lameck Banda, ananjatidwa  kamba koganizilidwa kuti anagonana ndi mtsikanayu ndi kumupatsa  pathupi kutsatira ndi momwe makolo amtsikanayu anakamang’alira kuti ndi wa […]

The post Wapulumuka pamene khoti lati msungwana amati anagona nayeyo simwana appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください