Wapolisi ku Thyolo wamwa magalasi pofuna kuzipha chifukwa choti anatentha mkazi wake ndi madzi owotcha. Wapolisiyi dzina lake ndi Constable Elson Mnyalira ndipo amagwira ku PMS G Division ku Thyolo. Mneneri wa apolisi mchigawo cha kum’mwera kwa kumvuma, a Edward Kabango atsimikiza za nkhaniyi. Malingana ndi Kabango, a Mnyalira anapita kumowa ndipo pobwera anakangana ndi […]
The post Wapolisi wamwa magalasi ku Thyolo appeared first on Malawi24.