M’mimba ndi nchipala: Apolisi m’boma la Mangochi akusakasaka mnyamata wina wa zaka 15 yemwe akuti wabaya pakhosi ndikupha mchemwali wake wa zaka 25 ati kamba koti amamukaniza kukazingira chimanga mu poto watsopano. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Mangochi a Amina Tepani Daudi omwe azindikira malemuwa ngati a Fyness Chapweteka omwe akumana […]
The post Wapha mchemwali wake kamba kapoto appeared first on Malawi 24.