Bambo wina wa zaka 32 zakubadwa akusungidwa mchitokosi cha apolisi ku Monkey-Bay m’boma la Mangochi kaamba komuganizira kuti wakhala akugwililira mwana wake wa zaka 12 mpaka kufika pomupatsa mimba. Alice Sichali yemwe ndi mneneri pa polisi ya Monkey-Bay wati bamboyu dzina lake ndi Moffat Phiri akumusunga mchitokosi kamba koti akumuganizira kuti wakhala akuchita zadama ndi […]
The post Wanjatidwa kaamba kogwililira mwana wake yemwe ndikumpatsa pathupi appeared first on Malawi 24.