Timu ya Mighty wanderers yagonjetsa timu ya Malawi Armed Forces College MAFCO 2-0 pa bwalo la Kamuzu mu TNM Super League. Chigoli chomwe chikhonza kukhala cha mwamsanga kwambiri chiyambileni League pa mphindi yachitatu mpira utangoyamba, osewela wakale wa Dedza Clement Nyondo ndi yemwe anapatitsa chitsogozo anyamata a Lali Lubani. Masewelowa anatenga mphamvu chigoli chitangobwera ndipo […]
The post Wanderers yaswa MAFCO pa Kamuzu, Songwe ikugawabe ma point appeared first on Malawi 24.