Ayi ndithu lero mu Tnm Super League zavutirapo ndithu pamene imodzi yokha ndiyo yaluza pamene ena anayi afanana mphamvu pakutha kwa masewero lero pa 11 May 2024. Mighty Mukuru Wanderers yamwa mkaka wa ngambwingambwi pomwe yaswa anyamata a Karonga United. Tikunena kuti Wanderers yaumbudza anyamata a Karonga United ndi chigoli chimodzi kwa duuu. Nayo Mafco […]
The post Wanderers yamwa wa mkaka appeared first on Malawi 24.