Mu masewelo a mpira wa miyendo okumbukira tsiku la mtsogoleri oyamba wa dziko lino a Ngwazi Dr Hastings Kamuzu Banda pakati pa Mighty Mukuru Wanderers ndi Silver Strikers pa Kamuzu stadium athela kukomera Wanderers. Mphunzitsi wa timu ya Silver Strikers, Peter Mponda wati masewero a alero sanali masewelo abwino kweni-kweni ponena kuti mipata yomwe anzawo anapeza […]
The post Wanderers yakong’ontha Silver Strikers appeared first on Malawi 24.