Mpira wamapazi ku Malawi: Timu yaing’ono ya Mighty Mukuru Wanderers yomwe makolo ake atuluka chakachi opanda chikho, imayenera kumenya ma “finals” awiri, ina ku Dowa ndi ina ku Machinga, Lamulungu likubwerali. Timu ya Wanderers Reserve Lamulungu likubwerali pa 31 December, 2023 imayenera kusewera ndime yotsiliza ndi timu ya Kalonga Rovers mu chikho cha King Kabvina […]
The post Wanderers yaing’ono imayenera kumenya ma “finals” awiri tsiku limodzi appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
