Wamisala adawona nkhondo: kapena JB ankanena zoona? Anthu akufusana za Onesimus

M’modzi mwa oyimba odziwika bwino m’dziko muno, Onesimus, wadzetsa manong’onong’o m’masamba a nchezo kaamba ka zovala zomwe anavala komaso kupezeka kwake ku phwando lomwe anakonza ndi yemwe amadziwika ndi za ‘umgochana’, Somizi. Somizi Mhlongo wa m’dziko la South Africa yemwe ndi muwulutsi wa pa wailesi ya kanema komaso ochita masewero, anapangitsa phwando loweluka pa 19 […]

The post Wamisala adawona nkhondo: kapena JB ankanena zoona? Anthu akufusana za Onesimus appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください