Walusa! Chakwera adzudzula ma kampane a zomanga manga kamba kochedwetsa ntchito

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wadzudzula ma kampane wena omwe amapatsidwa ntchito ya zomanga manga kuti akumachedwa kwambiri mukagwiridwe kawo ka ntchito. Mukulankhula kwawo, a Chakwera adati ndiwokhumudwa ndi m’mene ntchito zina za chitukuko zikuchedwera mdziko muno. A Chakwera alankhula izi lero boma la Rumphi komwe amatsekulira school zosula aziphuzitsi zomwe zamangidwa m’maboma […]

The post Walusa! Chakwera adzudzula ma kampane a zomanga manga kamba kochedwetsa ntchito appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください