Wakhwidzingiwa kamba kopezeka ndi wayilesi zakanema

Apolisi ku Kasungu akusunga mchitokosi njonda ina ya zaka 35 zakubadwa kamba kopezeka ndi katundu monga wayilesi za kanema zinayi za mtundu wa plasma ndipo njondayi ikuganiziridwa kuti idachita mokuba katunduyi. Wachiwiri kwa mneneli wa apolisi m’bomali a Miracle Mkozi, ati njondayi yomwe dzina lake ndi a Goodson Alli, idapezeka ndi katunduyu ku nyumba yake […]

The post Wakhwidzingiwa kamba kopezeka ndi wayilesi zakanema appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください