Kulitu nkhani ku bwalo uku. A Easter Gondwe omwe amatchuka ndi kukamba nkhani pa tsamba lino la Facebook akasumilidwa. Doro wa Zeze ndiye wakamang’ala kuti a Gondwe ndi a ‘hater’ ndipo amamudyola kwabasi. Akufuna abwalo awalipitse. Malinga ndi zikalata za ku bwalo zomwe Malawi24 yaona, a Dorothy Shonga amene nawonso amaziti ndi celebrity komanso ati […]
The post Wakamang’ala ku bwalo Doro wa Zeze: anandinamizira kuti ndinakwera bus pomwe ine ndinakwera ndege appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 