Wagwa mtengo ku St. Andrew’s Primary; pano fizi ndi K2.8 miliyoni yokha basi

…yolembetsera yokha ndi K372,750 Maphunziro ndi chuma kapena chuma ndi maphunziro abwino? Nzothekadi kuchepetsa mlingo wakusiyana pakati pa olemera ndi osawuka? Pomwe inu mukukanika kulipira K5000 kuti mwana wanu adziwe kunena kalenda-kalenda, afabeti ndi mavawelo, pano kalasi yotchipitsitsa ku St. Andrew’s International Primary School (SAIPS) ndi K750,000, akuti angokhwefula basi. Izi ndi malingana ndi uthenga […]

The post Wagwa mtengo ku St. Andrew’s Primary; pano fizi ndi K2.8 miliyoni yokha basi appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください