Vuto siinu a Malawi, vuto ndiife m’bomamu – Usi

…munthu wina akumathimitsa dala magetsi: awuza a Matola kuti asadzalireso Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha UTM, a Michael Usi, ati zinthu sizikuyenda bwino mdziko muno kaamba koti m’boma muli anthu ena oyipa, ndipo awuza nduna ya za mphamvu za magetsi ndi migodi a Ibrahim Matola kuti asadzalileso pankhani yakuthimathima kwa magetsi. A Usi omweso […]

The post Vuto siinu a Malawi, vuto ndiife m’bomamu – Usi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください