Vitumbiko Mumba wapita basi! BT CCAP yati ndiyokondwa ndi iyeyu chifukwa utsogoleri ulimo mwanyamatayi

Mmodzi wa anthu amene akufuna kupikisana nawo pa udindo wa wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha MCP a Vitumbiko Mumba walonjeza kuthandiza Blantyre CCAP Synod m’magawo osiyanasiyana. A Mumba ayankhula izi pa mpingo wa Mount Carmel CCAP mu mzinda wa Blantyre pamene adali nawo pa mwambo wolandira a Anderson Juma kukhala m’busa wa mpingowu. Mwazina, […]

The post Vitumbiko Mumba wapita basi! BT CCAP yati ndiyokondwa ndi iyeyu chifukwa utsogoleri ulimo mwanyamatayi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください