Vera wa zaka 10 ku Balaka akufunika thandizo la njinga yoyendera anthu a ulumali

Vera Kadwale wa zaka 10 yemwe amachokera m’mudzi wa Ngomano, Mfumu yaikulu Chimatiro  M’boma la Balaka ndipo salankhula komanso kuyenda akufunika thandizo la njinga yoyendera anthu a ulumali. Vera akukanika akusangalala ndi maufulu osiyanasiyana omwe ana anzake amakhala nawo monga  ufulu wa maphunziro ndi kusewera kamba kosowa njinga yoyendera anthu a ulumali. Vera, yemwe ali ndi […]

The post Vera wa zaka 10 ku Balaka akufunika thandizo la njinga yoyendera anthu a ulumali appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください