UTM ipikisana nawo mchisankho cha chaka chamawa, watero Patricia Kaliati

A Kaliati ati UTM idakali ya mphamvu mzigawo zonse za mdziko lino ngakhale mtsogoleri wawo a Saulos Chilima adamwalira pa ngozi ya ndege. Iwo ati akamaliza kukhuza maliro a Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu chipanichi chichititsa misokhano mzigawo zonse kuwuza Amalawi za tsogolo la chipanichi. “Mchipani chathu mukulowa anthu a zipani zosiyanasiyana kufuna […]

The post UTM ipikisana nawo mchisankho cha chaka chamawa, watero Patricia Kaliati appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください