UTM ikuti mgwirizano wawo ndi MCP ukadali chimodzimodzi

Chipani cha UTM chati mgwirizano wawo ndi MCP pa yemwe akudzaimira mgwirizano wa Tonse mu chisankho chikudzachi sudasinthe ndipo ‘udakali chimodzimodzi’. Mlembi wamkulu wa UTM, Patricia Kaliati, watiuza kuti adagawana zaka zisanu kwa otsogolera aliyense ndipo kuti mfundoyi sidachitike ndi atsogoleri a zipani ziwiri zokhazi ayi koma kuti otsatira ena adavomereza. Malingana ndi Kaliati, mgwirizanowu […]

The post UTM ikuti mgwirizano wawo ndi MCP ukadali chimodzimodzi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください