Mtsogoleri wa chipani cha UTM Michael Usi, omwenso ndiwachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, wadzudzula mlembi wa chipani chawo, a Patricia Kaliati kaamba kolankhura mosaganiza bwino. A Usi polankhura kwa otsatira chipanichi ku kunyumba ya boma ya Mudi anati uwu ndi mtudzu ndipo iwo salimbana nawo. “A Chilima pomwe amatisiya, anali m’boma, ine ndili m’boma […]
The post Usi akuti: “A Chilima pomwe amatisiya anali m’boma, ine ndili m’boma, ndiye zalakwika pati?” appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.